2 Mafumu 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Menahemu+ mwana wa Gadai, anachoka ku Tiriza+ kubwera ku Samariya n’kudzapha Salumu+ mwana wa Yabesi ku Samariyako. Kenako iye anayamba kulamulira m’malo mwake.
14 Ndiyeno Menahemu+ mwana wa Gadai, anachoka ku Tiriza+ kubwera ku Samariya n’kudzapha Salumu+ mwana wa Yabesi ku Samariyako. Kenako iye anayamba kulamulira m’malo mwake.