Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Deuteronomo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndinu amene mwayamba kuchititsa atumiki anu kuti aone ukulu wanu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene akuchita ntchito ngati zanu, ndiponso ntchito zamphamvu ngati zanu?+ Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndinu amene mwayamba kuchititsa atumiki anu kuti aone ukulu wanu+ ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene akuchita ntchito ngati zanu, ndiponso ntchito zamphamvu ngati zanu?+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+