-
1 Mbiri 13:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iye anauza mpingo wonse wa Isiraeli kuti: “Ngati mukuona kuti ndi bwino ndiponso ngati zili zovomerezeka kwa Yehova Mulungu wathu, tiyeni titumize uthenga kupita kwa abale athu ena m’madera onse a Isiraeli.+ Uthengawu upitenso kwa ansembe,+ ndi kwa Alevi,+ m’mizinda yawo+ yonse yokhala ndi malo odyetserako ziweto, kuti abwere kuno.
-