Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+ Numeri 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana aamuna a Perezi anali Hezironi+ amene anali kholo la banja la Ahezironi, ndi Hamuli+ amene anali kholo la banja la Ahamuli. Rute 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano uwu ndiwo mzere wa mbadwa za Perezi:+ Perezi anabereka Hezironi,+ Mateyu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+
12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+
21 Ana aamuna a Perezi anali Hezironi+ amene anali kholo la banja la Ahezironi, ndi Hamuli+ amene anali kholo la banja la Ahamuli.
3 Yuda anabereka Perezi+ ndi Zera, ndipo mayi awo anali Tamara.Perezi anabereka Hezironi.+Hezironi anabereka Ramu.+