10 Tsopano Yabezi anayamba kuitana Mulungu+ wa Isiraeli, kuti: “Mukandidalitsa+ ndi kukulitsa dziko langa,+ ndipo dzanja lanu+ likakhala nane, komanso mukanditeteza ku tsoka,+ kuti lisandivulaze,+ . . .” Choncho Mulungu anakwaniritsa zimene iye anapempha.+