Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea,+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake.

      Ichi chinali cholowa cha ana a Benjamini potsata mabanja awo.+

  • 1 Mafumu 2:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Pomaliza mfumu inatuma anthu kukaitana Simeyi,+ ndipo inamuuza kuti: “Udzimangire nyumba ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usachoke kumeneko kupita kwina ndi kwina.

  • Nehemiya 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mu Yerusalemu munalinso kukhala ena mwa ana a Yuda ndi ena mwa ana a Benjamini.+ Mwa ana a Yuda panali Ataya mwana wamwamuna wa Uziya amene anali mwana wa Zekariya. Zekariya anali mwana wa Amariya, Amariya anali mwana wa Sefatiya, Sefatiya anali mwana wa Mahalalele wochokera m’banja la Perezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena