1 Mafumu 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Yehova anene kwa ine n’zimene ndikalankhule.”+ Yeremiya 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova. Yeremiya 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo mneneri Yeremiya anawayankha kuti: “Ndamva zimene mwanenazo. Ndipemphera kwa Yehova Mulungu wanu malinga ndi zimene mwapempha.+ Ndipo mawu aliwonse amene Yehova angakuyankheni ndidzakuuzani.+ Sindidzakubisirani kalikonse.”+ Machitidwe 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti sindinakubisireni kanthu, koma ndinakuuzani chifuniro+ chonse cha Mulungu.
14 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Yehova anene kwa ine n’zimene ndikalankhule.”+
28 Mneneri amene walota maloto anene maloto akewo. Koma amene ndamuuza mawu anga, alankhule mawu angawo moona.”+ “Kodi mapesi a tirigu angafanane ndi tirigu weniweniyo?”+ watero Yehova.
4 Pamenepo mneneri Yeremiya anawayankha kuti: “Ndamva zimene mwanenazo. Ndipemphera kwa Yehova Mulungu wanu malinga ndi zimene mwapempha.+ Ndipo mawu aliwonse amene Yehova angakuyankheni ndidzakuuzani.+ Sindidzakubisirani kalikonse.”+