10 Chifukwa chakuti iweyo wagonjetsa+ Edomu, mtima wako wayamba kudzikuza.+ Sangalala ndi ulemu umene wapeza+ ndipo khala m’nyumba mwako momwemo. N’chifukwa chiyani ukufuna kumenya nkhondo+ pamene zinthu sizikukuyendera bwino?+ Iweyo ndi Ayuda amene uli nawowo mugonja.”