Levitiko 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika. Ezara 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano vomerezani+ machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, ndipo chitani zomusangalatsa+ ndi kudzipatula kwa anthu a mitundu ina ndiponso kwa akazi achilendo.”+
40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.
11 Tsopano vomerezani+ machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, ndipo chitani zomusangalatsa+ ndi kudzipatula kwa anthu a mitundu ina ndiponso kwa akazi achilendo.”+