Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 56:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 Yehova wanena kuti: “Anthu inu, tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama.+ Pakuti chipulumutso changa chatsala pang’ono kubwera,+ ndipo chilungamo changa chatsala pang’ono kuonekera.+

  • Akolose 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tikupemphereranso kuti muziyenda mogwirizana ndi zimene Yehova+ amafuna,+ kuti muzimukondweretsa pa chilichonse,+ pamene mukupitiriza kubala zipatso m’ntchito iliyonse yabwino, ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+

  • Aheberi 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 akukonzekeretseni ndi chilichonse chabwino kuti muchite chifuniro chake. Ndipo kudzera mwa Yesu Khristu, achite mwa ife zimene zili zokondweretsa pamaso pake.+ Kwa iye kukhale ulemerero kwamuyaya.+ Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena