Ekisodo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ ndi kuwauza kuti: “Sankhani nkhosa ndi mbuzi* malinga ndi mabanja anu, muiphere nsembe ya pasika.+ 2 Mbiri 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatero anapha nyama ya pasika+ pa tsiku la 14 la mwezi wachiwiri. Ansembe ndi Alevi anali atachititsidwa manyazi moti anadziyeretsa+ n’kubweretsa nsembe zopsereza kunyumba ya Yehova.
21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ ndi kuwauza kuti: “Sankhani nkhosa ndi mbuzi* malinga ndi mabanja anu, muiphere nsembe ya pasika.+
15 Atatero anapha nyama ya pasika+ pa tsiku la 14 la mwezi wachiwiri. Ansembe ndi Alevi anali atachititsidwa manyazi moti anadziyeretsa+ n’kubweretsa nsembe zopsereza kunyumba ya Yehova.