-
2 Mbiri 6:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 n’kubwerera kwa inu ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, m’dziko limene akukhalamo monga anthu ogwidwa,+ m’dziko la adani awo amene anawagwira ndiponso akapemphera kwa inu atayang’ana kudziko lawo limene munapatsa makolo awo, kumzinda umene mwasankha+ ndiponso kunyumba ya dzina lanu imene ndamangayi,+
-