1 Mafumu 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Solomo anaiyankha mfumukaziyo mafunso ake onse.+ Panalibe chimene mfumuyo inalephera kuyankha.+ Miyambo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+
5 Munthu wanzeru amamvetsera ndi kuphunzira malangizo owonjezereka,+ ndipo munthu womvetsa zinthu ndi amene amapeza nzeru zoyendetsera moyo wake,+