Numeri 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndilo dziko limene Yehova anagonjetsera+ khamu la Isiraeli. Dziko limeneli n’labwino kwa ziweto, ndipo atumiki anufe ziweto tili nazo.”+ 2 Mbiri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, Yehova anagonjetsa+ Aitiyopiyawo pamaso pa Asa ndi Ayuda, ndipo Aitiyopiyawo anayamba kuthawa.
4 ndilo dziko limene Yehova anagonjetsera+ khamu la Isiraeli. Dziko limeneli n’labwino kwa ziweto, ndipo atumiki anufe ziweto tili nazo.”+
12 Atatero, Yehova anagonjetsa+ Aitiyopiyawo pamaso pa Asa ndi Ayuda, ndipo Aitiyopiyawo anayamba kuthawa.