1 Mafumu 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anachotsa ngakhalenso agogo ake aakazi a Maaka+ pa udindo wawo wokhala mayi wa mfumu,+ chifukwa anapanga fano lonyansa kwambiri+ lopembedzera mzati wopatulika. Pambuyo pake Asa anagwetsa fanolo n’kukalitentha+ m’chigwa* cha Kidironi.+ 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano mantha+ a Yehova akugwireni.+ Samalani mmene mukuchitira+ chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+
13 Anachotsa ngakhalenso agogo ake aakazi a Maaka+ pa udindo wawo wokhala mayi wa mfumu,+ chifukwa anapanga fano lonyansa kwambiri+ lopembedzera mzati wopatulika. Pambuyo pake Asa anagwetsa fanolo n’kukalitentha+ m’chigwa* cha Kidironi.+
7 Tsopano mantha+ a Yehova akugwireni.+ Samalani mmene mukuchitira+ chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+