Ezara 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda. Ezara 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Akuluakuluwo anatiyankha kuti: ‘Ife ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi,+ ndipo tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga ndi kuimaliza.+ Ezara 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zonse zimene Mulungu wakumwamba+ walamula+ zokhudza nyumba yake, zichitike modzipereka kwambiri+ kuti mkwiyo usayakire dziko la mfumu ndiponso usayakire ana ake.+
2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti,+ ‘Yehova Mulungu wakumwamba+ wandipatsa+ maufumu onse a padziko lapansi. Iye wandituma kuti ndim’mangire nyumba ku Yerusalemu+ m’dziko la Yuda.
11 “Akuluakuluwo anatiyankha kuti: ‘Ife ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi,+ ndipo tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga ndi kuimaliza.+
23 Zonse zimene Mulungu wakumwamba+ walamula+ zokhudza nyumba yake, zichitike modzipereka kwambiri+ kuti mkwiyo usayakire dziko la mfumu ndiponso usayakire ana ake.+