Genesis 41:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+ Esitere 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumu inavula mphete yake yodindira+ imene inalanda Hamani ndi kuipereka kwa Moredekai. Pamenepo Esitere anaika Moredekai kuti ayang’anire nyumba ya Hamani.+ Danieli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+
42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+
2 Ndiyeno mfumu inavula mphete yake yodindira+ imene inalanda Hamani ndi kuipereka kwa Moredekai. Pamenepo Esitere anaika Moredekai kuti ayang’anire nyumba ya Hamani.+
17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+