Genesis 41:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+ Esitere 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo mfumu inavula mphete yodindira+ kudzanja lake ndi kuipereka kwa Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ amene anali kudana kwambiri ndi Ayuda.+ Danieli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+
42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+
10 Pamenepo mfumu inavula mphete yodindira+ kudzanja lake ndi kuipereka kwa Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ amene anali kudana kwambiri ndi Ayuda.+
17 Ndiyeno anabweretsa mwala ndi kutseka pakhomo la dzenjelo. Kenako mfumu inadinda mwalawo ndi mphete yake yodindira ndipo nduna zakenso zinaudinda ndi mphete yawo yodindira, kuti chilichonse chokhudza Danieli chisasinthidwe.+