Deuteronomo 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake. 2 Samueli 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+ Salimo 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+
36 Pakuti Yehova adzaweruza anthu ake,+Ndipo adzamva chisoni chifukwa cha atumiki ake,+Chifukwa adzaona kuti thandizo lawachokera.Adzaona kuti pangokhala munthu wonyozeka ndi wopanda pake.
41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+
11 Mwasintha kulira kwanga kuti kukhale kuvina.+Mwandivula chiguduli* changa ndipo mwandiveka chisangalalo,+