Esitere 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 N’chifukwa chake Ayuda akumidzi amene anali kukhala m’madera akutali ndi mzinda, anasandutsa tsiku la 14 la mwezi wa Adara+ kukhala tsiku lachikondwerero,+ laphwando, losangalala ndiponso tsiku+ lotumizirana chakudya.+ Luka 11:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma inu, perekani zimene zili mkati monga mphatso zachifundo,+ mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera.
19 N’chifukwa chake Ayuda akumidzi amene anali kukhala m’madera akutali ndi mzinda, anasandutsa tsiku la 14 la mwezi wa Adara+ kukhala tsiku lachikondwerero,+ laphwando, losangalala ndiponso tsiku+ lotumizirana chakudya.+
41 Koma inu, perekani zimene zili mkati monga mphatso zachifundo,+ mukatero zina zonse zokhudza inuyo zidzakhala zoyera.