Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 muziichitira zimene inafuna kuti zichitikire m’bale wakezo,+ ndipo muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Salimo 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+

      Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+

  • Salimo 37:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Lupanga lawo lidzalowa mumtima mwawo,+

      Ndipo mauta awo adzathyoka.+

  • Salimo 141:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Oipa onse adzagwera m’maukonde awo omwe,+

      Koma ine ndidzadutsa bwinobwino.

  • Danieli 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zitatero, mfumu inalamula kuti abweretse amuna amphamvu amene ananenera Danieli zoipa aja,+ ndipo anawabweretsadi. Kenako anawaponya m’dzenje la mikango+ pamodzi ndi ana awo ndi akazi awo.+ Iwo asanafike n’komwe pansi pa dzenjelo, mikango inawakhadzulakhadzula ndi kuphwanya mafupa awo onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena