Yesaya 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi wolima munda ndi pulawo amangokhalira kulima nthawi zonse,+ kuphwanya zibuma, ndi kusalaza dothi, osabzala mbewu?+
24 Kodi wolima munda ndi pulawo amangokhalira kulima nthawi zonse,+ kuphwanya zibuma, ndi kusalaza dothi, osabzala mbewu?+