Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Komabe ndikanakonda kulankhula ndi Wamphamvuyonse,+

      Ndikanasangalala ndikanatsutsana ndi Mulungu.

  • Yobu 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Bwenzi nditapita pamaso pake ndi nkhani yoti aweruze.

      M’kamwa mwanga bwenzi nditadzazamo mfundo zodziikira kumbuyo.

  • Yobu 31:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndikulakalaka ndikanakhala ndi wina wondimvetsera,+

      Kuti mogwirizana ndi chizindikiro changa chochita kulemba, Wamphamvuyonse andiyankhe.+

      Ndikulakalaka munthu amene ali nane pa mlandu akanalemba chikalata.

  • Aroma 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mwina unganene kwa ine kuti: “N’chifukwa chiyani Mulungu akupezabe anthu zifukwa? Kodi ndani angatsutse chifuniro chake chimene chinanenedwa?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena