Yobu 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikanadziwa kumene ndingamupeze,+Bwenzi nditapita kumalo kumene iye amakhala nthawi zonse.+ Yobu 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngati mmene ndinalili m’masiku amene ndinali mnyamata,+Pamene Mulungu anali bwenzi langa lapamtima, ndipo anali pahema wanga,+ Yobu 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndikulakalaka ndikanakhala ndi wina wondimvetsera,+Kuti mogwirizana ndi chizindikiro changa chochita kulemba, Wamphamvuyonse andiyankhe.+Ndikulakalaka munthu amene ali nane pa mlandu akanalemba chikalata.
4 Ngati mmene ndinalili m’masiku amene ndinali mnyamata,+Pamene Mulungu anali bwenzi langa lapamtima, ndipo anali pahema wanga,+ Yobu 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndikulakalaka ndikanakhala ndi wina wondimvetsera,+Kuti mogwirizana ndi chizindikiro changa chochita kulemba, Wamphamvuyonse andiyankhe.+Ndikulakalaka munthu amene ali nane pa mlandu akanalemba chikalata.
35 Ndikulakalaka ndikanakhala ndi wina wondimvetsera,+Kuti mogwirizana ndi chizindikiro changa chochita kulemba, Wamphamvuyonse andiyankhe.+Ndikulakalaka munthu amene ali nane pa mlandu akanalemba chikalata.