Yeremiya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Koma ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,+ cholakwa chako chidzaonekerabe ngati banga pamaso panga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Malaki 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndani adzapirire pa tsiku limene adzabwere?+ Ndipo ndani adzaime chilili iye akadzaonekera?+ Iye adzakhala ngati moto wa woyenga zitsulo+ komanso ngati sopo+ wa ochapa zovala.+
22 “‘Koma ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,+ cholakwa chako chidzaonekerabe ngati banga pamaso panga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
2 “Ndani adzapirire pa tsiku limene adzabwere?+ Ndipo ndani adzaime chilili iye akadzaonekera?+ Iye adzakhala ngati moto wa woyenga zitsulo+ komanso ngati sopo+ wa ochapa zovala.+