Yobu 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu mudzaitana ndipo ine ndidzayankha.+Mudzalakalaka ntchito ya manja anu. Salimo 138:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+ Yesaya 64:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+
8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+
8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+