Yohane 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira mwa ine, ngakhale amwalire, adzakhalanso ndi moyo.+ Machitidwe 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “N’chifukwa chiyani anthu inu mukuona ngati n’zosatheka kuti Mulungu aukitse akufa?+ 1 Akorinto 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ bwanji ena mwa inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa?+ Chivumbulutso 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyanja inapereka akufa amene anali mmenemo. Nayonso imfa ndi Manda zinapereka akufa+ amene anali mmenemo. Aliyense wa iwo anaweruzidwa malinga ndi ntchito zake.+
25 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndine kuuka ndi moyo.+ Aliyense wokhulupirira mwa ine, ngakhale amwalire, adzakhalanso ndi moyo.+
12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ bwanji ena mwa inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa?+
13 Nyanja inapereka akufa amene anali mmenemo. Nayonso imfa ndi Manda zinapereka akufa+ amene anali mmenemo. Aliyense wa iwo anaweruzidwa malinga ndi ntchito zake.+