Yobu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe ndikanakonda kulankhula ndi Wamphamvuyonse,+Ndikanasangalala ndikanatsutsana ndi Mulungu. Yobu 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chiweruzo chiperekedwe pakati pa mwamuna wamphamvu ndi Mulungu,Mofanana ndi pakati pa mwana wa munthu ndi mnzake.+
21 Chiweruzo chiperekedwe pakati pa mwamuna wamphamvu ndi Mulungu,Mofanana ndi pakati pa mwana wa munthu ndi mnzake.+