Salimo 145:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Ndipo ukulu wake ndi wosasanthulika.+ Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+ Chivumbulutso 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+
3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti: “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+