Yesaya 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+
26 M’tsiku limenelo,+ m’dziko la Yuda+ mudzaimbidwa nyimbo+ yakuti: “Ife tili ndi mzinda wolimba.+ Iye waika chipulumutso ngati mipanda ndiponso ngati chiunda chomenyerapo nkhondo.*+