Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 58:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Wolungama adzasangalala chifukwa chakuti waona oipa akupatsidwa chilango.+

      Adzasambitsa mapazi ake m’magazi a anthu oipa.+

  • Yesaya 37:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena:

      “Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza ndipo wakuseka.+

      Kumbuyo kwako, mwana wamkazi wa Yerusalemu wakupukusira mutu.+

  • Chivumbulutso 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena