2 Mafumu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena:“Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza+ ndipo wakuseka.+Kumbuyo kwako, mwana wamkazi wa Yerusalemu+ wakupukusira mutu.+
21 Awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena:“Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza+ ndipo wakuseka.+Kumbuyo kwako, mwana wamkazi wa Yerusalemu+ wakupukusira mutu.+