Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+ Salimo 65:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+ Chivumbulutso 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mngelo wachiwiri+ anathira mbale yake m’nyanja.+ Ndipo nyanja inasanduka magazi+ ngati a munthu wakufa, moti chamoyo chilichonse m’nyanjamo chinafa.+ Chivumbulutso 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mmodzi wa angelo 7 amene anali ndi mbale 7+ aja, anabwera n’kundiuza kuti: “Bwera, ndikuonetsa chiweruzo cha hule lalikulu+ lokhala pamadzi ambiri,+
3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
7 Iye akutontholetsa phokoso la nyanja,+Akutontholetsa phokoso la mafunde ake komanso chipwirikiti cha mitundu ya anthu.+
3 Mngelo wachiwiri+ anathira mbale yake m’nyanja.+ Ndipo nyanja inasanduka magazi+ ngati a munthu wakufa, moti chamoyo chilichonse m’nyanjamo chinafa.+
17 Mmodzi wa angelo 7 amene anali ndi mbale 7+ aja, anabwera n’kundiuza kuti: “Bwera, ndikuonetsa chiweruzo cha hule lalikulu+ lokhala pamadzi ambiri,+