Nehemiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino+ zonse zimene ndachitira anthu awa.+ Salimo 51:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chitirani Ziyoni zabwino mwa kukoma mtima kwanu.+Ndipo mangani mpanda wa Yerusalemu.+ Salimo 119:132 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 132 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima,+Mogwirizana ndi zigamulo zimene mumapereka kwa anthu okonda dzina lanu.+ Luka 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+
132 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima,+Mogwirizana ndi zigamulo zimene mumapereka kwa anthu okonda dzina lanu.+
14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba,+ ndipo pansi pano mtendere+ pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo.”+