Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Lidalitsike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+

      Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+

      Ame! Ame!*

  • Salimo 106:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndikumbukireni inu Yehova, ndipo ndisonyezeni kukoma mtima kumene mumasonyeza anthu anu.+

      Ndisamalireni ndi kundipulumutsa,+

  • Machitidwe 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+

  • Aheberi 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Mulungu si wosalungama woti angaiwale ntchito yanu ndi chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ mwa kutumikira oyera+ ndipo mukupitiriza kuwatumikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena