Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 33:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ chonde ndidziwitseni njira zanu,+ kuti ndikudziweni, kutinso mundikomere mtima. Ndipo kumbukirani kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+

  • Salimo 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+

      Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+

  • Salimo 86:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+

      Ndidzayenda m’choonadi chanu.+

      Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+

  • Salimo 143:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+

      Pakuti ndimadalira inu.+

      Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+

      Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena