Miyambo 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kupewa zoipa ndiko njira ya anthu owongoka mtima.+ Munthu amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+ Luka 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo anamuuza kuti: “Wayankha molondola. ‘Uzichita zimenezo, ndipo udzapeza moyo.’”+
17 Kupewa zoipa ndiko njira ya anthu owongoka mtima.+ Munthu amene amateteza njira yake, amasunga moyo wake.+