Miyambo 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndinadutsa pamunda pa munthu waulesi+ ndiponso pamunda wa mpesa wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+ Miyambo 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chitseko chimazungulira pomwe anachimangirira, ndipo waulesi amangotembenukatembenuka pabedi pake.+
30 Ndinadutsa pamunda pa munthu waulesi+ ndiponso pamunda wa mpesa wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+
14 Chitseko chimazungulira pomwe anachimangirira, ndipo waulesi amangotembenukatembenuka pabedi pake.+