Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+

      N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+

  • Salimo 119:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  72 Chilamulo+ chotuluka pakamwa panu n’chabwino kwa ine,+

      N’chabwino kwambiri kuposa ndalama masauzande zagolide ndi zasiliva.+

  • Salimo 119:127
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 127 N’chifukwa chake ine ndimakonda malamulo anu+

      Kuposa golide, golide woyenga bwino.+

  • Miyambo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 chifukwa kupeza nzeru monga phindu n’kwabwino kuposa kupeza siliva monga phindu, ndipo kukhala nazo monga zokolola n’kwabwino kuposa kukhala ndi golide.+

  • Miyambo 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kupeza nzeru n’kwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+

  • Miyambo 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pali golide komanso miyala yamtengo wapatali ya korali yambirimbiri, koma milomo yodziwa zinthu ndiyo ziwiya zamtengo wapatali.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena