Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo mfumu inavula mphete yodindira+ kudzanja lake ndi kuipereka kwa Hamani+ mwana wa Hamedata Mwagagi,+ amene anali kudana kwambiri ndi Ayuda.+

  • Esitere 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho Mfumu Ahasiwero inauza mfumukazi Esitere ndi Moredekai Myuda kuti: “Nyumba ya Hamani ndaipereka kwa Esitere,+ ndipo Hamani wapachikidwa pamtengo+ chifukwa chakuti anatambasula dzanja lake ndi kuukira Ayuda.

  • Esitere 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Izi zinali choncho chifukwa Hamani+ mwana wa Hamedata+ Mwagagi,+ amene anali kudana+ ndi Ayuda onse, anakonzera Ayudawo chiwembu kuti awawononge.+ Choncho iye anachita Puri+ kapena kuti Maere,+ ndi cholinga chakuti awasautse ndi kuwawononga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena