Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ndiyeno mukapitiriza kumvera zigamulo zimenezi ndi kuzisunga,+ Yehova Mulungu wanu adzasunga pangano+ ndi kukusonyezani kukoma mtima kosatha, zimene analumbirira makolo anu.+

  • Salimo 37:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+

      Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+

  • Salimo 37:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yehova amadziwa za moyo wa anthu osalakwa,+

      Ndipo cholowa chawo chidzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Salimo 37:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+

      Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+

  • Salimo 84:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+

      Iye amatikomera mtima ndi kutipatsa ulemerero.+

      Yehova samana anthu oyenda mosalakwa chinthu chilichonse chabwino.+

  • Miyambo 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’nyumba ya munthu wolungama muli katundu wambiri,+ koma katundu wa munthu woipa amabweretsa tsoka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena