1 Samueli 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Sauli anamukwiyira kwambiri+ Yonatani, ndipo anamuuza kuti: “Chimwana cha mkazi wopanduka iwe.+ Ukuganiza sindikudziwa kuti wasankha kugwirizana ndi mwana wa Jese, ndi kudzichititsa wekha manyazi ndiponso kuvula mayi ako?+ Salimo 123:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+
30 Ndiyeno Sauli anamukwiyira kwambiri+ Yonatani, ndipo anamuuza kuti: “Chimwana cha mkazi wopanduka iwe.+ Ukuganiza sindikudziwa kuti wasankha kugwirizana ndi mwana wa Jese, ndi kudzichititsa wekha manyazi ndiponso kuvula mayi ako?+
4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+