Chivumbulutso 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wina anatuluka m’nyumba yopatulika ya pakachisi, akufuula kwa wokhala pamtambo uja ndi mawu okweza, kuti: “Tsitsa chikwakwa chako ndi kuyamba kumweta,+ chifukwa ola la kumweta lafika.+ Pakuti zokolola za padziko lapansi zapsa bwino.”+ Chivumbulutso 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga+ lalitali lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu, ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Iye anali kupondapondanso m’chopondera mphesa+ cha mkwiyo waukulu wa Mulungu+ Wamphamvuyonse.
15 Mngelo wina anatuluka m’nyumba yopatulika ya pakachisi, akufuula kwa wokhala pamtambo uja ndi mawu okweza, kuti: “Tsitsa chikwakwa chako ndi kuyamba kumweta,+ chifukwa ola la kumweta lafika.+ Pakuti zokolola za padziko lapansi zapsa bwino.”+
15 M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga+ lalitali lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu, ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Iye anali kupondapondanso m’chopondera mphesa+ cha mkwiyo waukulu wa Mulungu+ Wamphamvuyonse.