Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 25:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “Ndiyeno iweyo, unenere mawu onsewa, ndipo anthuwo uwauze kuti, ‘Yehova adzabangula ngati mkango ali kumwamba,+ ndipo adzafuula ali kumalo ake oyera kumene amakhala.+ Iye adzabanguliradi malo ake okhalapo a padziko lapansi. Adzaimbira anthu onse okhala padziko lapansi nyimbo yofanana ndi imene anthu oponda mphesa amaimba.’+

  • Yoweli 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Yambani kumweta ndi chikwakwa,+ pakuti zokolola zacha.+ Bwerani, tsikirani kuno, pakuti moponderamo mphesa mwadzaza.+ Malo ogweramo vinyo wake asefukira, pakuti zoipa za anthu a mitundu ina zachuluka kwambiri.+

  • Chivumbulutso 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena