Deuteronomo 28:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Pamenepo moyo wako udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo udzakhala wamantha usiku ndi usana, moti sudzakhala wotsimikiza za moyo wako.+ 2 Mafumu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga+ ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+ Salimo 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anaona ndipo anadabwa.Anasokonezeka, moti anathawa mopanikizika kwambiri.+
66 Pamenepo moyo wako udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo udzakhala wamantha usiku ndi usana, moti sudzakhala wotsimikiza za moyo wako.+
26 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga+ ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+