2 Mafumu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga+ ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+
26 Anthu okhala m’mizindayo adzafooka manja.+Adzachita mantha kwambiri ndiponso adzachita manyazi.+Adzakhala ngati zomera zakutchire, ndi udzu wanthete wobiriwira,+Ngati udzu womera padenga+ ukawauka ndi mphepo yotentha yakum’mawa.+