29 “‘Ichi chidzakhala chizindikiro chanu:+ Chaka chino mudya mmera wa mbewu zimene zinagwera pansi.+ M’chaka chachiwiri mudzadya mbewu zongomera zokha, koma m’chaka chachitatu, anthu inu mudzabzale mbewu+ n’kukolola, ndipo mudzalime minda ya mpesa ndi kudya zipatso zake.+