Salimo 121:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Amene akuyang’anira Isiraeli,+Sangawodzere kapena kugona.+ Yesaya 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine Yehova ndine mlonda wa mundawo.+ Ndizidzauthirira nthawi zonse.+ Ndizidzaulondera usana ndi usiku kuti wina aliyense asauwononge.+
3 Ine Yehova ndine mlonda wa mundawo.+ Ndizidzauthirira nthawi zonse.+ Ndizidzaulondera usana ndi usiku kuti wina aliyense asauwononge.+