Numeri 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mose atatero, anakweza dzanja lake n’kumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Pamenepo madzi ambiri anayamba kutuluka, ndipo khamu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+ Nehemiya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munawapatsanso mkate wochokera kumwamba kuti athetse njala yawo.+ Munatulutsa madzi pathanthwe ndi kuwapatsa kuti athetse ludzu lawo,+ ndiyeno munawauza kuti alowe+ ndi kutenga dziko limene munalumbira mutakweza dzanja lanu kuti mudzawapatsa.+ Salimo 78:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anang’amba miyala m’chipululu+Kuti awapatse madzi akumwa ochuluka ngati a m’nyanja.+
11 Mose atatero, anakweza dzanja lake n’kumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Pamenepo madzi ambiri anayamba kutuluka, ndipo khamu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+
15 Munawapatsanso mkate wochokera kumwamba kuti athetse njala yawo.+ Munatulutsa madzi pathanthwe ndi kuwapatsa kuti athetse ludzu lawo,+ ndiyeno munawauza kuti alowe+ ndi kutenga dziko limene munalumbira mutakweza dzanja lanu kuti mudzawapatsa.+