Yoswa 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Patapita nthawi, ndinatenga Abulahamu+ tate wanu, kuchokera kutsidya lina la Mtsinje,+ ndipo ndinamuyendetsa m’dziko lonse la Kanani, ndi kuchulukitsa mbewu yake.+ Chotero ndinam’dalitsa ndipo anabereka Isaki,+ Mateyu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ndikukutsimikizirani kuti ambiri ochokera kum’mawa ndi kumadzulo+ adzabwera ndi kukhala patebulo limodzi ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo mu ufumu+ wakumwamba,+ Aroma 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+
3 “‘Patapita nthawi, ndinatenga Abulahamu+ tate wanu, kuchokera kutsidya lina la Mtsinje,+ ndipo ndinamuyendetsa m’dziko lonse la Kanani, ndi kuchulukitsa mbewu yake.+ Chotero ndinam’dalitsa ndipo anabereka Isaki,+
11 Koma ndikukutsimikizirani kuti ambiri ochokera kum’mawa ndi kumadzulo+ adzabwera ndi kukhala patebulo limodzi ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo mu ufumu+ wakumwamba,+
19 Ndiponso, ngakhale kuti chikhulupiriro chake sichinafooke, anaganizira za thupi lake, limene linali lakufa tsopano,+ popeza anali ndi zaka pafupifupi 100.+ Anaganiziranso zakuti Sara anali wosabereka.+